Zoopsa! Amangidwa kamba kotsatsa malonda a mwana womupeza wa zaka ziwiri

Apolisi m’boma la Zomba amanga a Chimwemwe Zololo chifukwa chofuna kugulitsa mwana wao wamwamuna omupeza wa zaka ziwiri. Wachiwiri kwa mneneri wa a polisi m’bomali a Aaron Chilala ati a Zololo amatsatsa malonda a mwanayo kwa mpondamatiki wina amene amachita malonda osiyanasiyana m’bomali. Malinga ndi a Chilala, mpondamatikiyu adatsina khutu apolisi za nkhaniyi ndipo apolisiwa […]

The post Zoopsa! Amangidwa kamba kotsatsa malonda a mwana womupeza wa zaka ziwiri appeared first on Malawi Nyasa Times – News from Malawi about Malawi.

マラウイニュースメルマガ登録

メルマガ限定配信のマラウイ超ローカルニュースが無料で受け取れます

マラウイ・アフリカ・国際協力に興味があったら登録しよう!

プライバシーポリシーについてはこちらを確認してください