Japan yapereka ndalama zoposa 1.99 biliyoni ku dziko la Malawi

Dziko la Japan lapereka ndalama zoposa 1.99 biliyoni kwacha kudziko la Malawi kudzera ku bungwe la UNICEF kuti zithandizire kuthana ndi ena mwamavuto omwe alipo m’madera ena omwe anakhudzidwa ndi Namondwe wa Freddy. Malinga ndi kalata yomwe Malawi24 yaona, yomwe atulutsa ndi a UNICEF, thandizoli lithandizira kulimbikitsa ntchito za umoyo, ukhondo komanso madzi m’maboma omwe […]

The post Japan yapereka ndalama zoposa 1.99 biliyoni ku dziko la Malawi appeared first on Malawi 24.

マラウイニュースメルマガ登録

メルマガ限定配信のマラウイ超ローカルニュースが無料で受け取れます

マラウイ・アフリカ・国際協力に興味があったら登録しよう!

プライバシーポリシーについてはこちらを確認してください