Zitengera a Malawi kukavotera mtsogoleri  wanzeru – Watero Lungu

M’tsogoleri wakale wa dziko la Zambia, a Edgar Chagwa Lungu, wati zitengera a Malawi kukavotera m’tsogoleri amene ndi wongoyeselera zinthu kapena wodziwa zinthu, maka pachisankho chomwe chichitike chaka chamawa m’dziko muno. A Lungu ayankhula izi pa tsamba lawo la m’chezo la Fesibuku dzulo pa 16 May 2024. M’mawu ake lungu anati akumva kuti a Malawi […]

The post Zitengera a Malawi kukavotera mtsogoleri  wanzeru – Watero Lungu appeared first on Malawi 24.

マラウイニュースメルマガ登録

メルマガ限定配信のマラウイ超ローカルニュースが無料で受け取れます

マラウイ・アフリカ・国際協力に興味があったら登録しよう!

プライバシーポリシーについてはこちらを確認してください