A Polisi m’boma la Balaka amanga bambo wina wazaka 38 kamba kokamiza nyamata wa zaka zisanu kuti amuseweretse ndi kumuyamwa maliseche ake. Malinga ndi kalata ya apolisi yomwe ikuzungulira m’masamba anchezo osiyanasiyana, bambo oganizilidwayu ndi a Kefasi Kambanizithe omwe achita kusaweluzikaku kumayambiliro kwa sabata ino m’mudzi mwa Harry. Kalata ya a Polisiyi ikusonyeza kuti bamboyi […]
The post Bambo wamangidwa kamba kokakamiza mnyamata kumuyamwa maliseche appeared first on Malawi 24.