President Lazarus Chakwera wati ukadaulo ndi ukatswiri mwa achinyamata ndiofunika kwambiri pa chitukuko cha dziko la Malawi. Pa chifukwa ichi, Chakwera wati mpofunika kuti maganizidwe akuya mdziko muno apatsidwe chilimbikitso chokwanira. Poyankhula pa mwambo okumbukira tsiku la luso ndi kufukula nzeru zozama, ku Bingu International Convention Centre (BICC) mu mzinda wa Lilongwe, Chakwera anatchula ma […]
The post Ukadaulo ndi ukatswiri ndi yankho ku Chitukuko- Chakwera appeared first on Malawi 24.