Pasipoti zathu zilibwino!- yatero Nthambi ya Immigration

Inu anthu omwe mumatuluka kunja kwa dziko lino tamverani! Nthambi ya lmmigration ndi Citizenship Services m’dziko muno yatsutsa mphekesera yoti ziphanso za dziko lino sizikuvomerezedwa pamabwalo ena okwelera ndege. Dipatimentiyi yanena izi lero kudzera mchikalata chomwe yatulutsa kutsatira mphekesera yomwe anthu ena akhala akufalitsa pa masamba amchezo ponena kuti ziphaso za dziko lino sizikuvomerezedwa pa […]

The post Pasipoti zathu zilibwino!- yatero Nthambi ya Immigration appeared first on Malawi 24.

マラウイニュースメルマガ登録

メルマガ限定配信のマラウイ超ローカルニュースが無料で受け取れます

マラウイ・アフリカ・国際協力に興味があったら登録しよう!

プライバシーポリシーについてはこちらを確認してください