Kaya wina afune, kaya asafune, 2025 ndikubweleranso m’boma – APM

Inu nonse amene a Peter Mutharika simukuwafuna, yang’anani kumbali. Nonse aja olemba kuti “APM my vote”, senderani chifupi. A Mutharika lero abwerezanso kuti chaka cha mawa akubwelera ku Sanjika. Mtsogoleri wa chipani chotsutsa cha DPP amene mmbuyomu amaoneka ngati wasiya za ndale asanalengezenso kuti basi akubwelera wauza anthu ku Mangochi kuti 2025 iye akuima ndipo […]

The post Kaya wina afune, kaya asafune, 2025 ndikubweleranso m’boma – APM appeared first on Malawi 24.

マラウイニュースメルマガ登録

メルマガ限定配信のマラウイ超ローカルニュースが無料で受け取れます

マラウイ・アフリカ・国際協力に興味があったら登録しよう!

プライバシーポリシーについてはこちらを確認してください