Osaletsa munthu odwala matenda a HIV ndi EDZI kumwa mankhwala – atero a chipembedzo

Chipembedzo ngati gawo lina lomwe limathandiza anthu omwe anapezeka ndi Matenda a HIV ndi EDZI kupitiliza kumwa mankhwala awo mwandondomeko, ati sibwino kuletsa  munthu odwala nthendayi kumwa mankhwala mwandondomeko. Mpingo wa Holy Trinity kudzera mwa Mneneri David Nkhondo wati ngati mtsogoleri yemwe amalandira komanso kukumana ndi anthu osiyanasiyana ndipo ena mwa iwo n’kukhala amene anapezeka […]

The post Osaletsa munthu odwala matenda a HIV ndi EDZI kumwa mankhwala – atero a chipembedzo appeared first on Malawi 24.

マラウイニュースメルマガ登録

メルマガ限定配信のマラウイ超ローカルニュースが無料で受け取れます

マラウイ・アフリカ・国際協力に興味があったら登録しよう!

プライバシーポリシーについてはこちらを確認してください