Nyimbo udayimba ndi Mafo ilikuti? Amalawi afunsa Gwamba

Amalawi adabwa ndikuchedwa kutuluka kwa Nyimbo yomwe Katswiri wachamba cha hip hop Gwamba adaimba ndi Madala Mafo mu chaka cha 2020. Gwamba adalonjeza mtundu wa Amalawi kuti ausa Mafo kwa akufa muchakachi. Ndipo adatsimikiza izi pa ma tsamba ake amchezo. Ngakhale adatero, pano talowa chaka chachiwiri Nyimbo yi isadatuluke. Ndipo izi zapangisa a Malawi kufusa […]

The post Nyimbo udayimba ndi Mafo ilikuti? Amalawi afunsa Gwamba appeared first on Malawi 24.

マラウイニュースメルマガ登録

メルマガ限定配信のマラウイ超ローカルニュースが無料で受け取れます

マラウイ・アフリカ・国際協力に興味があったら登録しよう!

プライバシーポリシーについてはこちらを確認してください

コメントを残す

メールアドレスが公開されることはありません。 が付いている欄は必須項目です