Nthambi ya zanyengo yati mvula iyamba February 1 ndipo igwa yambiri mwezi wonsewu

Nthambi yoona za kusitha kwanyengo  m’dziko muno yati pali chiyembekezo chachikulu kuti mvula iyamba kugwa mawa pa 1 February m’zigawo zonse za m’dziko muno. Wofalitsa nkhani Ku nthambiyi a Yobu Kachiwanda watsimikiza za izi ponena kuti zigawo zonse m’dziko muno zikuyembekezeka kuyamba kulandira mvula mwezi wa February. “Madera ambiri akuchigawo chapakati komanso ummwera kwa dziko […]

The post Nthambi ya zanyengo yati mvula iyamba February 1 ndipo igwa yambiri mwezi wonsewu appeared first on Malawi Nyasa Times – News from Malawi about Malawi.

マラウイニュースメルマガ登録

メルマガ限定配信のマラウイ超ローカルニュースが無料で受け取れます

マラウイ・アフリカ・国際協力に興味があったら登録しよう!

プライバシーポリシーについてはこちらを確認してください