Chakwera apempha a Malawi kuti asiye ndale zosungirana ka mpeni kumphasa

Mtsogoleri wa Dziko lino a Lazarus McCarthy Chakwera apempha a Malawi mdziko muno kuti asiye ndale zolozana dzala koma alimbikitse ndale zothandiza dziko. A Chakwera anena izi pa Bwalo la Zamasewera la Chinsapo pamsonkhano wa chitukuko. Asanapangitse msonkhano, a Chakwera adayendera kaye zitukuko zomwe zikuchitika mumzindawu. Zina mwa zitukuko zomwe anayendera ndi mlatho wa ndalama […]

The post Chakwera apempha a Malawi kuti asiye ndale zosungirana ka mpeni kumphasa appeared first on Malawi Nyasa Times – News from Malawi about Malawi.

マラウイニュースメルマガ登録

メルマガ限定配信のマラウイ超ローカルニュースが無料で受け取れます

マラウイ・アフリカ・国際協力に興味があったら登録しよう!

プライバシーポリシーについてはこちらを確認してください