Nthambi yoona za kusitha kwanyengo m’dziko muno yati pali chiyembekezo chachikulu kuti mvula iyamba kugwa mawa pa 1 February m’zigawo zonse za m’dziko muno. Wofalitsa nkhani Ku nthambiyi a Yobu Kachiwanda watsimikiza za izi ponena kuti zigawo zonse m’dziko muno zikuyembekezeka kuyamba kulandira mvula mwezi wa February. “Madera ambiri akuchigawo chapakati komanso ummwera kwa dziko […]
The post Nthambi ya zanyengo yati mvula iyamba February 1 ndipo igwa yambiri mwezi wonsewu appeared first on Malawi Nyasa Times – News from Malawi about Malawi.