Pomwe masiku akusenderabe kuchitseko kuti dziko lino lichititse chisankho chaka cha mawa chino, chipani cha Democratic Progressive (DPP) chataya ena mwa mavoti ophaipha, kamba koti anthu ena otsatira a Kondwani Nankhumwa, ati nawoso atuluka nchipani ndipo dzuwa lili phwee, ang’amba nsalu za chipanichi. Lamulungu pa 28 January, 2024, a Nankhumwa omwe posachedwapa pamodzi ndi anzawo […]
The post Ngati achotsa Nankhumwa, achotsanso ife – mamembala ang’amba nsalu za DPP appeared first on Malawi 24.