Madera ena ku Nkhata-Bay mawayilesi samveka

Anthu okwana pafupifupi 7,200 okhala m’madera ena akumidzi  m’boma la Nkhata-Bay alibe mwayi opeza mauthenga osiyanasiyana kudzera pa wailesi popeza mawayilesi samveka kumaderawa kuyambira nthawi ya atsamunda. Madera monga Thotho, Mangw’ina, Musinjiyiwi, Chisangawe, Masasa, Chitundu komanso Sanji a Madera la mfumu yaikulu Khodza adakali mu mdima pa nkhani yokhudza ma mayilesi  komanso makina a intaneti. […]

The post Madera ena ku Nkhata-Bay mawayilesi samveka appeared first on Malawi 24.

マラウイニュースメルマガ登録

メルマガ限定配信のマラウイ超ローカルニュースが無料で受け取れます

マラウイ・アフリカ・国際協力に興味があったら登録しよう!

プライバシーポリシーについてはこちらを確認してください