Ndakufikitsani ku Canaan — Chakwera

Mtsogoleri wa dziko lino a Lazarus Chakwera anena kuti akwanitsa kale kuchita zambiri zomwe iwo anawalonjeza a Malawi mu nthawi ya kampeni. A Chakwera anena izi lero ku nyumba ya chifumu ya Kamuzu mu mzinda wa Lilongwe pa mwambo omwe amalandila ndalama kuchokela ku African Development Bank. Malingana ndi a Chakwera, iwo analonjeza za ulamuliro […]

The post Ndakufikitsani ku Canaan — Chakwera appeared first on Malawi 24.

マラウイニュースメルマガ登録

メルマガ限定配信のマラウイ超ローカルニュースが無料で受け取れます

マラウイ・アフリカ・国際協力に興味があったら登録しよう!

プライバシーポリシーについてはこちらを確認してください

コメントを残す

メールアドレスが公開されることはありません。 が付いている欄は必須項目です