Mwana wafa ku Machinga atadya nsima ya gaga

Mwana  wa zaka zisanu ndi ziwiri wafa pomwe wina akulandira thandizo la mankhwala pa chipatala cha Machinga atadya nsima yomwe anaphikira gaga m’mudzi wa Makangata. Mwana yemwe wamwalirayo dzina lake ndi Yamikani Witness wa m’mudzi wa mfumu yaikulu Nkoola. Wapampando wachitukuko ku Makangata wauza nyumba zofalitsa nkhani kuti anthu asanu ndi m’modzi  anayamba kusanza komanso […]

The post Mwana wafa ku Machinga atadya nsima ya gaga appeared first on Malawi 24.

マラウイニュースメルマガ登録

メルマガ限定配信のマラウイ超ローカルニュースが無料で受け取れます

マラウイ・アフリカ・国際協力に興味があったら登録しよう!

プライバシーポリシーについてはこちらを確認してください