Mwana wa zaka zisanu ndi ziwiri wafa pomwe wina akulandira thandizo la mankhwala pa chipatala cha Machinga atadya nsima yomwe anaphikira gaga m’mudzi wa Makangata. Mwana yemwe wamwalirayo dzina lake ndi Yamikani Witness wa m’mudzi wa mfumu yaikulu Nkoola. Wapampando wachitukuko ku Makangata wauza nyumba zofalitsa nkhani kuti anthu asanu ndi m’modzi anayamba kusanza komanso […]
The post Mwana wafa ku Machinga atadya nsima ya gaga appeared first on Malawi 24.