Mtsogoleri wa dziko lino Lazarus Chakwera wati sibwino kunamiza aMalawi kuti dziko likhonza kumangidwa popanda maziko ovuta komanso a misozi, ndipo kulankhula motha mawu otere ndi chifukwa choti omwe adali m’boma m’mbuyomu adaba ndipo palibe akuwalondola nde akuwona kuti nzophweka kungomanga dziko mwachidule. Polankhula pa mwambo okhazikitsa zipangizo za makono za ulimi ku BICC mu […]
The post Musandilankhulitse Pambali – Chakwera appeared first on Malawi 24.