Unduna wa za umoyo wati m’boma la Mchinji mwagwa muliri wa matenda a chikuku omwe pano agwira anthu asanu ndi awiri (7) m’bomali. Malingana ndi kalata yomwe wasayinira ndi mkulu wa zaumoyo m’bomali, Dr Yohane Mwale, pakadali pano mulili m’mudzi mwa Mtiwa m’dera la Chamveka, mfumu yayikulu Simphasi wachulukira. Kalatayi ikusonyeza kuti pa 12 April […]
The post Mulili wa chikuku wabuka m’boma la Mchinji appeared first on Malawi 24.