Mulandira malipiro anu mochedwerako, atero akuluakulu a ADMARC

Bungwe la Agriculture Development and Marketing Corporation (ADMARC) lalemba kalata kuwuza anthu ogwira ntchito ku bungweli kuti adekhe kaamba kakuti mwezi uno alandira malipiro awo mochedwerako chifukwa cha mavuto azachuma omwe akuta bungweli. Malingana ndi a Ethel Zilirakhasu omwe ndi mkulu owona za anthu ogwira ntchito ku bungweri ati chuma sichikuyenda bwino ku bungweli koma […]

The post Mulandira malipiro anu mochedwerako, atero akuluakulu a ADMARC appeared first on Malawi 24.

マラウイニュースメルマガ登録

メルマガ限定配信のマラウイ超ローカルニュースが無料で受け取れます

マラウイ・アフリカ・国際協力に興味があったら登録しよう!

プライバシーポリシーについてはこちらを確認してください

コメントを残す

メールアドレスが公開されることはありません。 が付いている欄は必須項目です