MP Noel Lipipa wa DPP akuti zokamba za a Chakwera ndi zomwe zili mu bajeti zikusemphana

Phungu wa chipani cha DPP ku Blantyre City South Noel Lipipa wati zomwe anayankhula mtsogoleri wa dziko lino Lazarus Chakwera mu SONA chaka chino ndi zomwe zili mu ndondomeko ya zachuma ya chaka chino mzosagwirizana komanso mzosatheka. Izi zadza pomwe aphungu akupitilizabe kuikapo ndemanga zawo pa ndondomeko ya za chuma ya chaka chino yomwe inapelekedwa […]

The post MP Noel Lipipa wa DPP akuti zokamba za a Chakwera ndi zomwe zili mu bajeti zikusemphana appeared first on Malawi Nyasa Times – News from Malawi about Malawi.

マラウイニュースメルマガ登録

メルマガ限定配信のマラウイ超ローカルニュースが無料で受け取れます

マラウイ・アフリカ・国際協力に興味があったら登録しよう!

プライバシーポリシーについてはこちらを確認してください