Mnyamata wapezeka atamwalira mu nyumba ya chibwenzi ku Phalombe

Mnyamata wa mu folomu yachiwiri pa sukulu ina ya sekondale ku Phalombe wapezeka atafa ku nyumba ya chibwenzi chake komwe anakagona. Apolisi a ku Phalombe atsimikiza za nkhaniyi ndipo ati mnyamatayu dzina lake ndi Joseph Madeya yemwe amachokera m’mudzi wa Ntchedzinga, mfumu yaikulu Mkanda ku Mulanje. Malingana ndi oyankhulira apolisi ku Phalombe, a Jimmy Kapanja, […]

The post Mnyamata wapezeka atamwalira mu nyumba ya chibwenzi ku Phalombe appeared first on Malawi24.

close

マラウイニュースメルマガ登録

メルマガ限定配信のマラウイ超ローカルニュースが無料で受け取れます

マラウイ・アフリカ・国際協力に興味があったら登録しよう!

プライバシーポリシーについてはこちらを確認してください

Generated by Feedzy