Mlonda wanjatidwa ataba zida zoyimbira m’tchalitchi chomwe amalondera

A polisi munzinda wa Lilongwe akusunga mchitokosi mlonda wa zaka 44 wa mpingo wa Time of God pomuganizira kuti anathyola kachisicho ndi kuba zida zoyimbira za ndalama zoposa K3.5 miliyoni.  Wofalitsa nkhani za polisi ya Lilongwe a Hastings Chigalu, atsimikiza za nkhaniyi ndipo azindikira oganiziridwayu ngati a Patrick Zgambo omwe akuti anapanga chipongwechi kumayambiliro a […]

The post Mlonda wanjatidwa ataba zida zoyimbira m’tchalitchi chomwe amalondera appeared first on Malawi 24.

マラウイニュースメルマガ登録

メルマガ限定配信のマラウイ超ローカルニュースが無料で受け取れます

マラウイ・アフリカ・国際協力に興味があったら登録しよう!

プライバシーポリシーについてはこちらを確認してください