Mkaidi awulura momwe analowetsera mafoni awiri m’matumbo mwake

Mkaidi yemwe lachitatu anadabwitsa anthu kaamba kopezeka ndi mafoni awiri m’matumbo mwake kundende ya Zomba, wati analowetsa mafoniwa kudzera ku malo ochitila chimbudzi ndipo waulura kuti akaidi ambiri ali ndi anthu omwe amawapititsira mafoniwa kundendeko. Mkaidiyu yemwe dzina lake ndi Frank Siposi, lachitatu pa 11 May, 2022, m’mimba mwake munapezeka mafoni awiri othobwanya koma anyuwani, […]

The post Mkaidi awulura momwe analowetsera mafoni awiri m’matumbo mwake appeared first on Malawi 24.

マラウイニュースメルマガ登録

メルマガ限定配信のマラウイ超ローカルニュースが無料で受け取れます

マラウイ・アフリカ・国際協力に興味があったら登録しよう!

プライバシーポリシーについてはこちらを確認してください

コメントを残す

メールアドレスが公開されることはありません。 が付いている欄は必須項目です