Ngati njira imodzi yowonetsetsetsa kuti anthu ambiri mdziko muno ali ndi chiphaso cha unzika chomwe chingawathandizile kulembetsa mu kaundula wa voti, bungwe la Malawi Electoral Commission (MEC) liri ndi malingaliro opeleka zipangizo za Biometric Voter Registration Kits (BVRKs) ku bungwe lowona za kalembera la National Registration Bureau (NRB). Malingana ndi chikalata chomwe wasainila ndi mkulu […]
The post MEC ipeleka zipangizo za BVRKs ku bungwe la NRB appeared first on Malawi 24.