Malawi ali patsogolo pankhani yoteteza Njovu

Bungwe la Elephant Protection Initiative (EPI) lati dziko la Malawi lachita bwino pa nkhani yoteteza njovu ndipo laposa maiko oposa 24 amchigawo cha Africa omwe ali pansi pa bungweli. Poyankhulapo pa za nkhaniyi ndi wailesi ina yofalitsa mawu dziko muno, Nkulu wa Parks and Wildlife, a Brighton Kumchedwa ati njira monga kukhazikitsidwa kwa ndondomeko ya National […]

The post Malawi ali patsogolo pankhani yoteteza Njovu appeared first on Malawi 24.

マラウイニュースメルマガ登録

メルマガ限定配信のマラウイ超ローカルニュースが無料で受け取れます

マラウイ・アフリカ・国際協力に興味があったら登録しよう!

プライバシーポリシーについてはこちらを確認してください