Anthu okwana pafupifupi 7,200 okhala m’madera ena akumidzi m’boma la Nkhata-Bay alibe mwayi opeza mauthenga osiyanasiyana kudzera pa wailesi popeza mawayilesi samveka kumaderawa kuyambira nthawi ya atsamunda. Madera monga Thotho, Mangw’ina, Musinjiyiwi, Chisangawe, Masasa, Chitundu komanso Sanji a Madera la mfumu yaikulu Khodza adakali mu mdima pa nkhani yokhudza ma mayilesi komanso makina a intaneti. […]
The post Madera ena ku Nkhata-Bay mawayilesi samveka appeared first on Malawi 24.