Kubweretsa mafuta pa sitima yapamtunda kutha kupangitsa kuti mtengo utsike

Bungwe la Petroleum Importers Limited (PIL) lati kuyamba  kubweretsa mafuta pa sitima yapamtunda kutha kupangitsa kuti mtengo wamafuta utsike m’dziko muno. Mkulu wa kampani ya Petroleum Importers Limited m’dziko muno a Martin Msimuko ndiwomwe anena idzi poyankhula ndi Malawi24. A Msimuko ati kubweretsa mafuta pa Sitima yapa njanji ndikothandiza kwambiri chifukwa mafuta amabwera ochuluka nthawi […]

The post Kubweretsa mafuta pa sitima yapamtunda kutha kupangitsa kuti mtengo utsike appeared first on Malawi 24.

マラウイニュースメルマガ登録

メルマガ限定配信のマラウイ超ローカルニュースが無料で受け取れます

マラウイ・アフリカ・国際協力に興味があったら登録しよう!

プライバシーポリシーについてはこちらを確認してください

コメントを残す

メールアドレスが公開されることはありません。 が付いている欄は必須項目です