Chipani chotsutsa cha DPP chasambwadza akuluakulu a Kongeresi ndi UTM kuti ndi osadziwa kanthu. A chipanichi ati utsogoleri wa Tonse ndi osapatsa chikoka ndipo atsogoleri ake ndi zidebe chabe zopanda kanthu koma phokoso basi. Malinga ndi chikalata chimene chipanichi chatulutsa potsatira kafukufuku wa Afrobarometer amene waonetsa kuti a Malawi ochuluka akufinyika kamba ka utsogoleri wa […]
The post Koma a Tonse ndiye ndi zidebe zenizeni, Chakwera alongeze azipita – DPP yatsukuluza Tonse appeared first on Malawi 24.