Nonse othodwa ndi zipani zonse zilipo pano, ena chabe ongokhala okondwa ndi bambo Kondwani Nankhumwa ndipo mumafunitsitsa atalamula dziko lino, musataye mtima kwenikweni. Chipani chatsopano chikubwela. Okamba akuti ndi cha a Kondwani Nankhumwa. Dzina lake ndi PDP, People’s Development Party. Malinga ndi Malipoti amene Malawi24 yamvetsedwa, ma mulumuzana ena amene anali a chipani cha DPP […]
The post Malipoti akuti Nankhumwa akubwela ndi chake chipani: PDP appeared first on Malawi 24.