Kutsatira ulosi omwe nthambi yoona za nyengo mdziko muno inachita ponena kuti mvula iyamba kugwa pa 1 February mwezi uno, tsopano a Malawi ambili ayamikila ulosi wanthambiyi pamene mvula yagwadi m’madera ochuluka ngati momwe nthambiyi inaloselela. Dzana mneneri wa ku nthambi yoona za nyengo a Yobu Kachiwanda anatsimikizira mtundu wa a Malawi ponena kuti mvula […]
The post Khwimbi latayira kamtengo Yobu Kachiwanda ndi DCCMS ulosi wamvula utapherezera appeared first on Malawi 24.