Apolisi ku Mulanje anjata njonda ziwiri zomwe zakhala zikuzinganiziridwa kuti zakhala zikuchita za umbanda mbomali. Mneneri wa apolisi ku Mulanje a Innocent Moses watsimikiza za nkhaniyi ndipo iye wati njonda ziwiri mayina awo ndi a Richard Semu azaka 36 zakubadwa komanso a Joseph Elton azaka 32. Nkhani yonse ikuti apolisi m’bomali anatsinidwa khutu ndi anthu […]
The post Akanganya awili omwe akhala akuchita za umbanda ku Mulanje awanjata appeared first on Malawi 24.