A Malawi omwe anabayitsa katemera wa AstraZeneca pofuna kupewa mulili wa Covid19 ayamba kukhala mwa mantha pomwe kampani yomwe imapanga katemerayu yauza khothi kuti pali kuthekera kuti katemera wawoyu, nthawi zina, atha kuyambitsa zovuta zina mthupi mwa munthu. Nkhaniyi ikubwera pomwe anthu okwana makumi asanu ndi m’modzi (51) anakasumira kampani ya AstraZeneca ponena kuti katemera […]
The post Kampani ya AstraZeneca yavomera kuti katemera wake wa Covid-19 atha kuyambitsa mavuto ena mthupi appeared first on Malawi 24.