Kalindo adzudzulidwa kamba kofuna kuti Chizuma achotsedwe ntchito

Anthu ena m’dziko muno akupitilira kudzudzula zomwe wayankhula Bon Kalindo posachedwapa kuti mkulu wa bungwe lothana ndi katangale la ACB, a Martha Chizuma, achotsedwe ntchito. Nkhaniyi ikudza pomwe posachedwapa bwalo la milandu mu mzinda wa Mzuzu mwezi uno lalamura kuti apolisi afufuze nkhani yoti a Chizuma anauza munthu wina zinsinsi za ntchito yawo zomwe samayenera […]

The post Kalindo adzudzulidwa kamba kofuna kuti Chizuma achotsedwe ntchito appeared first on Malawi 24.

マラウイニュースメルマガ登録

メルマガ限定配信のマラウイ超ローカルニュースが無料で受け取れます

マラウイ・アフリカ・国際協力に興味があったら登録しよう!

プライバシーポリシーについてはこちらを確認してください

コメントを残す

メールアドレスが公開されることはありません。 が付いている欄は必須項目です