Bwato satsitsilana pakati pa nyanja — Usi

Wachiwiri kwa pulezidenti wa chipani cha UTM a Michael Usi omwenso ndi nduna ya zokopa alendo achenjeza zipani za Malawi Congress Party (MCP) ndi UTM kuti wina asatsitse nzake mu bwato pakati pa nyanja. A Usi amayankhula izi dzulo pa mwambo okumbukila mtsogoleri woyamba wa dziko lino a Kamuzu Banda. Ku mwambowu kunalinso mtsogoleri wa […]

The post Bwato satsitsilana pakati pa nyanja — Usi appeared first on Malawi 24.

close

マラウイニュースメルマガ登録

メルマガ限定配信のマラウイ超ローカルニュースが無料で受け取れます

マラウイ・アフリカ・国際協力に興味があったら登録しよう!

プライバシーポリシーについてはこちらを確認してください

コメントを残す

メールアドレスが公開されることはありません。