Pamene anthu asanamalize kusimba za woyimba Jetu yemwe amachokera ku Bangwe munzinda wa Blantyre, woyimba winanso ochokera ku delari, Zonke Too Fresh, walowa m’bwalo ndi nyimbo yake ya tsopano yomwe akuyitchula kuti ‘Vote’. Zonke Too Fresh, yemwe dzina lake leni leni ndi Zaithwa Mhone, watulutsa nyimbo yatsopanoyi Lachiwiri m’mawa ndipo nyimboyi yatulutsidwa pamodzi ndi kanema […]
The post Bangwe yadya wani, Zonke watekesa ndi nyimbo ya tsopano appeared first on Malawi 24.