Anthu awili afa ndipo ena avulala pangozi yagalimoto yomwe yachitika lero pamudzi wa Machinga mboma la Dowa munsewu wa Salima-Lilongwe pamene galimoto yomwe anakwera inalephera kukwera chitunda zomwe zinapangitsa kubwerelambuyo mpaka kukagwera ku phompho. Mneneri wa apolisi ya Dowa Alice Sitima watsimikiza za ngoziyi ndipo wati anthu awiri afawa ndi a Mathews Nekhantani a zaka […]
The post Anthu awili afa galimoto litagwera ku phompho appeared first on Malawi 24.