Kazembe wa dziko la Amerika m’dziko muno, David Young, watsanzika potsatira kutha kwa nthawi yake ya ukazembe. Mu chikalata chomwe ofesi ya ukazembe wa dziko la Ameleka yatulutsa chati a David akhala pa udindo wa ukazembe kwa zaka 34 ndipo tsopano apum. Mu mawu awo, a Young ati ndi okondwa kuti atumikira anthu a dziko […]
The post A David Young atsanzika appeared first on Malawi 24.