A Chakwera sanauze Ukraine ndi Russia kuti azimenyana, atero a Mkaka

Mlembi wamkulu wa chipani cha Malawi Congress Party (MCP), a Eisenhower Mkaka ati mavuto ena omwe anthu m’dziko muno akukumana nawo anayamba chifukwa cha nkhondo ya pakati pa Ukraine ndi Russia ndipo ndikulakwa kumanena kuti mavutowa abwera ndi Mtsogoleri wa dziko lino a Lazarus Chakwera poti a Chakwera sanauze Ukraine ndi Russia kuti azimenyana. A […]

The post A Chakwera sanauze Ukraine ndi Russia kuti azimenyana, atero a Mkaka appeared first on Malawi 24.

マラウイニュースメルマガ登録

メルマガ限定配信のマラウイ超ローカルニュースが無料で受け取れます

マラウイ・アフリカ・国際協力に興味があったら登録しよう!

プライバシーポリシーについてはこちらを確認してください

コメントを残す

メールアドレスが公開されることはありません。 が付いている欄は必須項目です