Chipembedzo ngati gawo lina lomwe limathandiza anthu omwe anapezeka ndi Matenda a HIV ndi EDZI kupitiliza kumwa mankhwala awo mwandondomeko, ati sibwino kuletsa munthu odwala nthendayi kumwa mankhwala mwandondomeko. Mpingo wa Holy Trinity kudzera mwa Mneneri David Nkhondo wati ngati mtsogoleri yemwe amalandira komanso kukumana ndi anthu osiyanasiyana ndipo ena mwa iwo n’kukhala amene anapezeka […]
The post Osaletsa munthu odwala matenda a HIV ndi EDZI kumwa mankhwala – atero a chipembedzo appeared first on Malawi 24.