Boma kudzera ku nthambi ya polisi, lakaniza a Malawi kukachita m’bindikilo pa Chingeni komaso Kalinyeke pomwe eni magalimoto akumapeleka ndalama akamadutsa ponena kuti kutero ndi kuphwanya malamulo adziko lino. Izi ndimalingana ndichikalata chomwe nthambi ya polisi yatulutsa Lachisanu pa 21 January chomwe wasainira ndi ofalitsa nkhani wankulu wa polisi a James Kadadzera omwe awuza anthu […]
The post Tithana ndi aliyese ochita m’bindikilo pa Chingeni, Kalinyeke – atero apolisi appeared first on Malawi 24.