Mbava zowombera mwini nyumba zagwidwa ku Blantyre

 A bambo atatu ku Soche mu nzinda wa Blantyre, ali manja mwa apolisi kamba kowombera ndi mfuti mwini nyumba yomwe anapita kukaba. Watsimikiza za nkhaniyi ndi wachiwiri kwa ofalitsa nkhani pa polisi ya Soche a Hopeness Potani omwe azindikira mbavazi ngati a Madalitso Mthupi azaka 34, Mike Davie a zaka 28 komaso a Gift John […]

The post Mbava zowombera mwini nyumba zagwidwa ku Blantyre appeared first on Malawi 24.

マラウイニュースメルマガ登録

メルマガ限定配信のマラウイ超ローカルニュースが無料で受け取れます

マラウイ・アフリカ・国際協力に興味があったら登録しよう!

プライバシーポリシーについてはこちらを確認してください