Wapolisi waombera chibwezi naye nkuziphanso

Wapolisi wina m’boma la Dedza wapha bwenzi lake pomuombera ndi mfuti ndipo nayeso wadzipha podziombera ndi mfuti yomweyo. Malingana ndi ma lipoti omwe tsamba lino lapeza, mtsikanayu yemwe dzina lake ndi Sabina, wawomberedwa ndi bwenzi lakeyu, Sergeant Paul Mpheluka, m’mawa wa lero Lachitatu pa 3 April. Malipoti osatsimikizika akusonyeza kuti usiku wa Lachiwiri Sabina amamwa […]

The post Wapolisi waombera chibwezi naye nkuziphanso appeared first on Malawi 24.

マラウイニュースメルマガ登録

メルマガ限定配信のマラウイ超ローカルニュースが無料で受け取れます

マラウイ・アフリカ・国際協力に興味があったら登録しよう!

プライバシーポリシーについてはこちらを確認してください