Pomwe anthu ochuluka analavula za ku khosi zitaoneka kuti oyimba Tay Grin wasiyana ndi bwezi lake la m’dziko la Zambia, Mutale Mwanza, awiriwa ali limodzi ku United Kingdom, ndipo gulu langoti kukamwa yasa kwinaku manja ali ku nkhongo, osakhulupilira zomwe awona. Mwezi watha, pa masamba a m’chezo, panali pokopoko kamba ka uthenga wina omwe Mwanza […]
The post Tay Grin ali ku UK ndi Mutale Mwanza appeared first on Malawi 24.