Mpungwepungwe unakula m’nyumba ya malamulo pamene mbali ya boma yavomereza lamulo kuti ulimi wachamba udzilimidwa m’dziko muno. Izi zinadzetsa mpungwepungwe kunyumbayi pamene aphungu achipani chotsutsa cha Democratic Progressive Party (DPP) anati sakugwirizana ndi lamuloli. Izi zinapangitsa aphungu achipanichi kutuluka pa zokambilanazi ati kusonyeza kusakondwa ndi lamulori. Ngakhale aphunguwa anatuluka panja, nyumbayi inavomereza za biloyi ndipo […]
The post Aphungu adutsitsa chamba appeared first on Malawi 24.