Khansala wa dera la Mzalangwe ku Mzimba Hora, a Dani Nkosi watuluka chipani cha DPP ndipo walowa chipani cha AFORD. Poyankhula atalandiridwa ndi akuluakulu achipani cha AFORD, Nkosi wati walowa chipanichi ndicholinga choti chigawo chakumpoto kwa dziko lino nako kukhale chipani champhamvu. A Nkosi ati izi zichititsa kuti chigawo chakumpoto chikhale ndi zitukuko zolozeka monga […]
The post Khansala wa DPP wazitaya ku Mzimba Hora, walowa chipani cha Aford appeared first on Malawi Nyasa Times – News from Malawi about Malawi.