Tiyeni tigwirane manja pothana ndi mchitidwe ochitira ana nkhanza ana achichepere ku nkhaza, watero Bushiri

Prophet Shepherd Bushiri watsindika kufunika kogwirana manja pothana ndi mchitidwe ochitira nkhaza ana ndi cholinga chokwanilitsa masomphenya a dziko lino pa chitukuko. Mneneri Bushiri wanena izi masanawa pomwe amagula katundu osiyanasiyana wa mwana wa mmudzi mwa mndola Mfumu yaikulu Kambwiri m’boma la Salima yemwe anadyetsedwa dowe wamuwisi ngati chilango kwa iye. Malinga ndi a Bushiri […]

The post Tiyeni tigwirane manja pothana ndi mchitidwe ochitira ana nkhanza ana achichepere ku nkhaza, watero Bushiri appeared first on Malawi Nyasa Times – News from Malawi about Malawi.

マラウイニュースメルマガ登録

メルマガ限定配信のマラウイ超ローカルニュースが無料で受け取れます

マラウイ・アフリカ・国際協力に興味があったら登録しよう!

プライバシーポリシーについてはこちらを確認してください