M’nkuthwanima kwa diso, oyimba Emmie Deebo yemwe anali ndiomutsata ongokwana m’manjamu pa tsamba lake la fesibuku, tsopano wamusadabuza Patience Namadingo yemwe anali oyimba otsatidwa kwambiri kuno ku mpanje kamba koti pano msungwanayu akutsatidwa ndi anthu 1.7 miliyoni kutsatira kugulilidwa masamba ena a kunja a fesibuku. Kampani yothandiza anthu a luso ya Akometsi yomweso imamuthandiza Emmie […]
The post Emmie Deebo wagulilidwa masamba pa fesibuku, pano ali ndiomutsata 1.7 miliyoni appeared first on Malawi 24.