Bwanjinso? Aford yayimitsa msonkhano wake waukulu

Chipani cha Alliance for Democracy (AFORD) chayimitsa msonkhano wake waukulu omwe umayenera kuchitika mu mwezi wa Epulo mpaka sabata yoyamba ya Julayi chaka chino, ponena kuti akadakachitabe zina zokonzekera. Polankhula, mtsogoleri wa chipanichi a Enock Chihana wati mwa zina, pali akulu akulu ena omwe akhale akulowa mchipanichi posachedwapa, ndipo akufuna kupereka mpata kwa anthu otere […]

The post Bwanjinso? Aford yayimitsa msonkhano wake waukulu appeared first on Malawi Nyasa Times – News from Malawi about Malawi.

マラウイニュースメルマガ登録

メルマガ限定配信のマラウイ超ローカルニュースが無料で受け取れます

マラウイ・アフリカ・国際協力に興味があったら登録しよう!

プライバシーポリシーについてはこちらを確認してください