Mtsogoleri wa chipani cha Democratic Progressive Party (DPP) yemwenso ndi mtsogoleri wakale wa dziko lino, a Peter Mutharika, lero anakachezera asilamu pa mzikiti wa Mangochi Main Mosque mu town ya Mangochi. Mtsogoleri wakaleyu anapita kukachezera asilamuwa pamene ali m’nyengo yosala kudya ya Ramadan. Polankhula, a Mutharika adati nyengo ya Ramadan ndiyofunikila kwambiri chifukwa nthawiyi imawayandikitsa […]
The post Mutharika achezera asilamu ku Mangochi appeared first on Malawi 24.